Pala
Zimbili Dlamini
Catherine Groenewald

Zama anali kukonzekela kuyenda kusukulu.

1

Atate anali kupika pala yakuseni.

2

"Amai aziba kupika pala yabwino kwambili!" anati Zama.

3

Zama imamupasa mpamvu zakusukuku pala.

4

Pala yapya.

5

Atate aika mukaka ndipo asekelela.

6

"Atate pala iyi ifunika yina shuga," anati Zama.

7

"Pala yopika amai niyabwino kupambana yamene apika atate," Zama anaganiza.

8

"Atate, nipempako shuga," anati Zama.

9

Atate ake zama anamupasa shuga inangu.

10

"Mmu! Atate! Munali mwaika mcele wambili mu pala!"

11

"Atate nanga amai azabwela ntawi bwanji?" Zama anafunsa.

12
You are free to download, copy, translate or adapt this story and use the illustrations as long as you attribute in the following way:
Pala
Author - Zimbili Dlamini, Hlengiwe Zondi
Translation - Bether Mwale Moyo
Illustration - Catherine Groenewald
Language - CiNyanja
Level - First words