

Naka ndi Nala akhala pansi pa mtengo m'tchire louma.
Nala akumva kuwuluzika kwa masamba ouma kamba ka kuputa kwa kamphepo.
"Tamvera Naka. Ukuwamva masambawo?" afunsa Nala.
"Inde, nanenso ndikuwamva komanso ndikuwaona akuwuluzika.
"Ukukumbukira chimene chimachititsa masamba kuti aziwuluzika?" afunsa Naka.
"Ndipamene mphepo ikuulutsa zinthu," ayankha Nala.
"Ndikuwona ngati ndi mpweya," atero Naka.
"Mpweya uli paliponse, koma sitimawuwona..." Nala ayamba kufotokoza.
Naka amudula mzakeyo, nati, "Koma timaona ndi kumva masamba akamawuluzika!"
Nala continues, “We can’t see air, but we can see and hear the effects of air moving. That’s called wind.â€
“Wind is air?!†Naka asks.
“Yes,†smiles Nala.
She adds, “Air also holds tiny water drops in clouds. When the water in clouds gets too heavy, water drops fall as rain.â€
“Imagine us rising into the sky in a hot air balloon. The balloon is like a water drop, the air holds it up,†says Nala.
“We also breathe air,†remembers Naka.
“Yes, all animals and plants need air,†says Nala.
“We need clean air,†agrees Naka.
“We can’t see air, but what is it made of?†asks Naka.
“Air is a mix of gases and tiny bits of dust,†replies Nala.
“The earth is wrapped in air,†says Nala.
“Air is all around us. The earth’s air stretches from here into space,†she adds.
——Questions


