Mabatani
Nahyuha Sarah
African Storybook

Mabatani anga onse ndi ozungulira.

1

Ena mwa mabatani anga ndi obiriwira.

2

Mabatani anga onse ndi ang'onoang'ono.

3

Ena mwa mabatani anga ndi achikasu.

4

Mabatani anga onse ndi abwino.

5

Ena mwa mabatani anga ndi ofiira.

6

Mabatani anga onse ndi onyezimira.

7

Ena mwa mabatani anga ndi abulu.

8

Mabatani anga onse ndi abwino.

9

Ndimawakonda mabatani anga onse.

10
You are free to download, copy, translate or adapt this story and use the illustrations as long as you attribute in the following way:
Mabatani
Author - Nahyuha Sarah, Kukiriza Deborah, Wamigambe Brenda
Translation - Peter Msaka
Illustration - African Storybook, Natalie Propa, Wiehan de Jager
Language - ChiChewa
Level - First sentences