Banja la Maria
Little Zebra Books
Leo Daly

Ndine Maria.

1

Awa ndi mayi anga.

2

Uyu ndiye mwana wa kwathu.

3

Awa ndi bambo anga.

4

Uyu ndi m'chimwene wanga.

5

Uyu ndi m'chemwali wanga.

6

Awa ndi agogo anga aakazi.

7

Awa ndi agogo anga aamuna.

8

Awa ndi amalume anga.

9

Awa ndi azakhali anga.

10

Banja lathu!

11
You are free to download, copy, translate or adapt this story and use the illustrations as long as you attribute in the following way:
Banja la Maria
Author - Little Zebra Books
Translation - Little Zebra Books
Illustration - Leo Daly, Magriet Brink
Language - Cinyanja (Mozambique)
Level - First sentences