Ng'ombe yatu Pendo
Ruth Odondi
Rob Owen

Uyu ni Ndalo.

1

Ndalo akonda kuwelenga.

2

Uyu ni Pendo.

3

Pendo akonda kudya makaloti.

4

Ndalo akacoka ku sukulu amapeleka Pendo mukudyesela.

5

Amamupasa Pendo manzi akumwa.

6

Atate amamupasa gaga Pendo.

7

Amamukama mukaka masiku onse Pendo.

8

Pendo ali namukaka kwambili.

9

Atate amagulisa mukaka wa Pendo.

10

Ndalo amamwa mukaka masiku onse.

11

Ndalo amakamba kuti, "Zikomo Pendo!"

12
You are free to download, copy, translate or adapt this story and use the illustrations as long as you attribute in the following way:
Ng'ombe yatu Pendo
Author - Ruth Odondi
Translation - Bether Mwale Moyo, Milimo Vision
Illustration - Rob Owen
Language - CiNyanja
Level - First words