Cona ndi Cule anali kukhala pa mudzi wocedwa Cinsamba.
Mudzi wa Cinsamba unali mudzi wa congo komanso wamaonekedwe abwino.
Iwo anali kukonda ndiyo za masamba ndipo anali kukondana kwambiri.
Nthawi ina anakumana ndi bwenzi wina dzina lake Coza.
Cona ndi Cule anauza Coza kuti ayambe kukhala pamodzi.
Coza sanataye nthawi koma anabvomera.
Cona anauza Cule kuti amange nyumba ya Coza.
Onse atatu anayamba kukhala pamodzi mwa cisangalalo.