

Panali sikulu lina lochedwa mtumayo.sikulu iyi inalikupezeka pa mudzi wochedwa kalavula gaga.
Pasukulu pomwepo ana asukulu ana kuchita bwino zamuma phunziro zao,cifukwa anali kupita kaka phunzirila kumalo osayina- siyana ndi ana akuma sukul
Tsikulina aphunzitsi akulu wa pa sukulu iyo ana uza ana ao APA sukulu iyo kuti apite kumanyumba
Yao akakonzeko ulendo womwe azakhala nao,wama phunziro.
Tsiku yaulendo ina kwana,ndipo ana ana ana konzeka mokwana bwino-bwino cifukwa anaweren
Anapita pamalo ochedwa kamvi.Malo away yanali molo yokoma kwambiri,ngkhale ana asukulu aja anawa kinda kwambiri.
Ana asukulu anafika bwino pa kamvi.Ana aja sanafune kuti akhale pansi kuti aphumule,anafuna kuti
ayanganile malo ya kamvi cifuk
Pamwe anali kuzungulila malo ya kamvi ana asukulu,panali ana asanu omwe anatuluka pagula la anzao napita kwaokha.
Ana aja anapita paka kuchile komwe anayamba kusewele mpaka kunawadela.pa ana asanu awa panali Matha,Petelu,Maliya,Monde
ndi Di
Aphunzitsi awo,anayamba kusakila mpaka kunala,ndipo aphunzitsi anadankhawa."Anagniza kuti ana awa anga pits kuti kuno popeza malo ano ndi kuyamba kubwelako"
Cinali cinthu covuta kwambiri kuti apeze ana aja omwe ana sowa.Mpakani analepela ku
Ana asanu aja omwe anathawa kupanda ulayila,anasowela kotelo kuti anakondwa kwambiri muchile muja anali kusewelera.pomwe anatha usewela,anafuna kuti spite komwe achokela kuliabwenzi awo,koma codabwisa nicakuti sana kumbukile komwa anacokela
Matha anali yemwe analumidwa ndi njoka,koma abwenzi aske sana ziwe cocita mpaka Maths iya ana mwalila,muchilemo ndimomwe anashika thupi lake.
Tsiku lina pomwe anapitiliza kusakila njira kuti apeze komwe kunali ana asukulu anzao analili,ana kumana ndi Bambi yaswa.
Pomwe anafika pamalo ya kamvi,sana wapeze ana asukulu anzao kapena aphunzitsi. Anthu aja ana bwerelamo Ku manyumba ao.
Panali cinthu cimodzi come China dabwisa kolo LA Matha.kholo ija inafunsa," kodi Matha alikuti,popeza kuti aphunzitsi anakamba kuti alipomodzi ndi inu.
Thupi la Matha linatengedwa ndi kupelekedwa kumudzi kwamakolo,komwe anashikila.
Kucokela tsiku iya kunalibenso mwana wasukulu omwe anacita zimeneizi cifukwa cakuti ana ambiri anatengelapo phunziro yaikulu kwambiri.

