

Agogo anyamula madzi.
Amalume Anagula basi dzulo.
Cola ici ndi cabwino.
Munthu aliyense ali ndi diso lopenyera.
Elina ali kuwelenga mau amcinyanja.
Fupa langa ndi lolimba kwambiri monga nsimbi.
Galimoto langa limathamanga kwambiri.
Uyu ndi bulu.
Impala imapezeka kuchire.
Ng'ombe za amalume zili pa Joko.
Kaingo ali ndi mawanga-mawanga.
Ili ndi lilime.
Gawa undi ndi mfumu ya acewa.
Nthoci imapatsa thanzi ku thupi.
Kwakhala ola limodzi kuti ndipite kusukulu.
Mona wateleka poto waukulu pamoto.
Dzenera ya nyumba yathu ilingana ndi shepu ya rekitangulo.
Mkwinda ndi imodzi mwamasukulu a impact network.
Mwatisakha akonda kumwa tiyi m'mawa muli monse.
Udzu umakula kwambiri.
Tiyi nthawi zonse timabvudula ndi sipuni.
Thomasi akuyatsa wailesi yakanema.
Atate apita kumudzi ndi galimoto.
Izi ndi zina Mwa ziweto zomwè timasunga pa nyumba yanthu.

