Buku la mapatani
Impactnetwork Brandina Banda

Kodi mukuona anthu angati ali pamthuthuthu.

1

Nanga mnyamata ndi mtsikana Ali kucita ciani?

2

Nanga apolisi ali apa abvala ciani. Kodi ndi mpolosi wamkazi kapena wamuna.

3

Taonani mzibambo ali kumenya mnyamata. Kodi I imeneyi sinkhanza kodi?

4

Amai ali kusambika mwana.Mwana ali mu dishi.

5

Maria ndi yohane akwera bulu.

6

Mtsikana uyu ndi wokongola kwambiri ndipo alupesa tsitsi pogwiritsa nchito kalilole kudziyang'anira.

7

Amaonje abvala khoti kuopa kuti angabvumbwe ndi mvula.

8

Mnyamata ali kusamba kumanja pofuna kuteteza matenda osiya-siyana.

9

Mateyo ali kupalasa njinga atanyamula katundu.

10

Matulina ali kutsuka ndiwo zamasamba.

11

Abambo Wakale ali kugela tsitsi.

12

Garu alikufuna kulima mwana wa bambo sitolo, bambo sitolo ali kuteteza mwana.

13

Azibambo awiri alikuyang'ana galimoto lomwe yaonongeka.

14

Mnyamata wocepa wanyamula katundu wolemera

15
You are free to download, copy, translate or adapt this story and use the illustrations as long as you attribute in the following way:
Buku la mapatani
Author - Impactnetwork Brandina Banda
Illustration -
Language - CiNyanja
Level - First paragraphs