Aa Amai abeleka mwana.
Bb Iyi ndi bola.
Cc Onani cona.
Dd Dzani ndi yamsipu.
Ee Uyu mtsikana ndi Elina.
Ff Fisi ali matoto.
Gg Ana akwera galimoto.
Hh Honda Ili ndi mawiro awiri.
Ii Mnyamata aimba ng'oma.
Jj Iyi ndi juzi.
Kk Uyu ndi kalango wa njinga.
Ll Uyu ndi loko.
Mm Maluwa awa ali ndi utoto wabwino.
Nn Nsimbi iyi itchisa bwino.
Oo Ona atsikana awa abvina kwambiri.
Pp Iyi pani aphikiramo.
Ss Sitolo iyi ndi zakudya zokoma.
Tt Tambala uyu ali ndi mendo yatali-tali.
Uu Uka pa bedi apa.
Vv Vinyu waikidwa mkapu.
Ww Wezulu imalizidwa pampira.
Y y Njira yopita kumunda ndi yonkhota-nkhota.
Zz Kumwendo kuli zala zisanu.