

Aa / Agogo.
Awa ndi agogo
Bb
Buluku.
Buluku iyi ndi yakale.
Cc / Cola.
Cola ici anacigula dzulo.
Dd/ Delesi.
Delesi iyi ndi ya Lumbiwe.
Ee/Enala.
Enala ndi mtsikana wa liwiro.
F/f.
Fupa la nkhuku ndi lofewa.
Gg.
Gome iyi timadyerapo cakudya.
Hh.
Hatchi imalumpha kwambiri.
Ii.
Insa ndi nyama yocenjera.
Jj.
Asilikali amavala jombo.
Kk.
Atsibweni anagula wailesi ya kanema.
Ll.
Lilime lake ndi lotupa.
Mm.
Mausi ndi yoyendetsera mlozi.
Nn.
Nunji ili ndi minga mthupi lake.
Oo
Ovolosi iyi ili ndi mabatani.
Pp
Uyu ndi poto wophikamo nsima.
Rr
Roko wolimba umatiteteza ku mbala.
Ss
Sopo wosambira mthupi ndi wofunikira kwambiri.
Tt
Tomato wathu wakula kudimba.
Uu
Ici ndi cizindikiro ca ulalo.
Vv
Vinyu uyi ndi waukali zedi.
Ww
Atate anagula wailesi.
Yy
Dziko ndi yozungulira.
Zz
Izi ndi zovala za mwana.

