Kalulu athandiza
Impact Network and Anderson Phiri

Panali Agondwe ndi Akazi ao,Jesi ndi kalulu .Anthu awa amakhala pa famu.

1

Agondwe ndi akazi ao anali ndi mwana m'modzi wa mkazi.Mwana uyu anali wosalankhula koma wokongola.

2

Tsiku lina Jesi anakumana ndi kanyama kena kochedawa kalulu ndipo kalulu anagwa mmcikondi ndi mtsikana .Jesi kuti amkwatire.Koma Jesi amangobvomera ndi mutu cifukwa sanali kulankhula pa kugwirizana ndi kalulu.

3
You are free to download, copy, translate or adapt this story and use the illustrations as long as you attribute in the following way:
Kalulu athandiza
Author - Impact Network and Anderson Phiri
Illustration -
Language - CiNyanja
Level - First paragraphs