

Aa
Amai asenza mtsuko wa madzi.
Bb
Abusa amawerenga baibulo kuchalichi.
Cc
Patsiku la sabata timapita ku chalichi ukapemphera.
Dd
Dabwitso amatapila madzi mu dilamu.
Ee
Eliya aseweretsa galimoto yamawaya.
Ff
Foni ya agogo ndiya utoto oyera.
Gg
Gunduzani anagula gome kwa a menyani.
Hh
Hosi ndi nyama imene imathamanga kwambiri.
Ii
Insa ndi nyama yamthengo imene ilingana ndi mbuzi.
Ji
Jekete la state ndi labwino kwambiri.
Kk
Khasu la agogo ndilakuthwa kwambiri.
Ll
Lambi ya amalume ndi ya gilasi.
Mm
Mpando uyu unapangidwa ndi atate.
Nn
Nyumba ya amalume ndi ya malata.
Oo
Olipa ali kusinja cimanga mum'tondo.
Pp
Poto uyu ndiwabwino kwambiri.
Rr
Rabisoni wanyamula cola cakusukulu.
Ss
Sompho ya Malizani ndiyakuthwa kwambiri.
Tt
Thadza la apongozi ndi labwino kwambiri.
Uu
Ufa uli msaka.
Vv
Vaileti ali kupsyera.
Ww
Wailesi yomwe anagula amalume ndiyabwino kwambiri.
Yy
Yohane ndi mnyamata waukhondo kwambiri.
Zz
Zelipa ali kuuluza cimanga ndi licelo.

