Maina a zinthu
Impact network Rabecca. L. Tembo

Uyu ndi mtsikana.

1

Uyu ndi mnyamata.

2

Uyu ndi mwana.

3

Iyu ndi poto.

4

Uyu ndi mtondo.

5

Uyu ndi moto.

6

Uyu ndi mpeni.

7

Uyu ndi sopo.

8

Uyu ndi Tambala.

9

Uyu ndi Cona.

10

Uyu ndi uta.

11

Uyu ndi mwezi.

12

Uyu ndi mtsuko.

13

Uyu ndi Galu.

14

Iyi ndi Nsomba.

15

Iyi ndi njinga.

16
You are free to download, copy, translate or adapt this story and use the illustrations as long as you attribute in the following way:
Maina a zinthu
Author - Impact network Rabecca. L. Tembo
Illustration -
Language - CiNyanja
Level - First paragraphs