Onani nsima ndi ndiyo ya nkhuku.
Onani mnyamata ali kumenya mpila wa minyendo.
Onani mtsikana akuphika nsima.
Onani amai akulima.
Onani banga.
Onani galimoto.
Onani nkhuku.
Onani poto uli pamoto.
Onani mbalame ili ku uluka.
Onani nthochi yakupsa.
Onani Mnyamata akusamba.
Onani ng'ombe ili kudya udzu.
Onani nsomba ili m'madzi.
Onani Mtsikana wasenza madzi.
Onani lalanje.
Onani bakha ili m'madzi.
Onani Mnyamata ali kuthamanga.
Onani akakowa.
Onani gwawa
Onani nyama ya m'thengo.