

Kodi utha kuona ciani?
Nditha kuona thebulo.
Kodi utha kuona ciani?
Nditha kuona cinanazi.
Kodi utha kuona ciani?
Nditha kuona apo.
Kodi utha kuona ciani?
Nditha kuona mpeni.
Kodi utha kuona ciani?
Nditha kuona mtengo.
Kodi utha kuona ciani?
Nditha kuona cimate.
Kodi utha kuona ciani?
Nditha kuona poto.
Kodi utha kuona ciani?
Nditha kuona delesi.
Kodi utha kuona ciani?
Nditha kuona mtondo.
Kodi utha kuona ciani?
Nditha kuona khasu.
Kodi utha kuona ciani?
Nditha kuona kabudula.
Kodi utha kuona ciani?
Nditha kuona papaya.
Kodi utha kuona ciani?
Nditha kuona kaloti.
Kodi utha kuona ciani?
Nditha kuona dzungu.
Kodi utha kuona ciani?
Nditha kuona moto.
Kodi utha kuona ciani
Nditha kuona nyumba
Kodi utha kuona ciani?
Nditha kuona ketulo.
Kodi utha kuona ciani?
Nditha kuona bvwembe.
Kodi utha kuona ciani?
Nditha kuona buku.

