ZINTHU ZOKONDEKA-BUKU LA PATANI
IMPACT NETWORK and KAMWENGO SAKALA

Ndimakonda kulemba.

1

Ndimakonda ku bvina.

2

Ndimakonda kudya.

3

Ndimakonda masewera olimbitsa thupi.

4

Ndimakonda kuceza ndi anzanga.

5

Ndimakonda nchito yanga yoteteza anthu.

6

Ndimakonda kusoka zobvala.

7

Ndimakonda ku phika.

8

Ndimakonda ku sewera ndi anzanga.

9

Ndimakonda Kunene ndakatulo.

10

Ndimakonda nchito yotuta mcenga.

11

Ndimakonda kupemphera.

12

Ndimakonda kutsuka mbale.

13

Ndimakonda kuthamanga kukawerenga mabuku.

14

Ndimakonda kudula nkhuni.

15

Ndimakonda kutunga madzi.

16
You are free to download, copy, translate or adapt this story and use the illustrations as long as you attribute in the following way:
ZINTHU ZOKONDEKA-BUKU LA PATANI
Author - IMPACT NETWORK and KAMWENGO SAKALA
Illustration -
Language - CiNyanja
Level - First paragraphs