Ndimakonda ku kwela njinga.
Ndimakonda ku senga mkaka.
Ndimakonda
Ndimakonda kuotha moto.
Ndimakonda kupita ku sukulu.
Ndimakonda kutapa madzi.
Ndimakonda kusewera mpira wa minyendo.
Ndimakonda kusambila.
Ndimakonda kucapa zobvala.
Ndimakonda ku phunzira.
Ndimakonda kumvetsera ku Nthano za agogo m'madzulo.
Ndimakonda kutsuka ziwiya.
Ndimakonda ku thamanga.
Ndimakonda ku dula nkhuni.
Ndimakonda ku kwela bulu.