Yohane akonda kusewera.
Yohane akonda ukhwapa udzu.
Yohane akonda kapu.
Yohane akonda kuwerenga.
Yohane akonda kuwedza nsomba.
Yohane akonda kulima.
Yohane akonda poto wake.
Yohane akonda kunyamula bokosi ya sopo.
Yohane akonda kudya.
Yohane akonda kumanga nyumba.
Yohane akonda galu wake.
Yohane akonda kuyendetsa njinga.
Yohane akonda kuotha moto.
Yohane akonda kuphika nsima.
Yohane akonda kuyenda monyada.
Yohane akonda kuumba mbiya.
Yohane akonda kuthamanga.
Yohane akonda kubvina.
Yohane akonda kusamba kumanja.
Yohane akonda kusesa.