Onani mnyamata akumenya mpira Wa miyendo.
Onani kangalu akusewera ndi mwana wake.
Onani atate akusuzila pa dzenera ya nyumba.
Onani mtsikana wanyamula cola.
Onani mnyamata aotha moto.
Onani poto pamoto.
Onani agogo ali kuyenda.
Onani nyama ikudya udzu.
Onani mtengo wagwa.
Onani galu akulowa kudzenje.
Onani bakha pamadzi.
Onani mbalame zakaka.