Uyu ndi Maliseni .Maliseni ali kusuta fodya.
Uyu ndi Maliseni.Ali ndi mzace akumenya mpila.
Uyu ndi Maliseni.Ali ndi mzace ali kupatsana cakudya.
Uyu ndi Maliseni .Ali kuwerenga buku.
Uyu ndi Maliseni .Ali kupita kusukulu.
Uyu ndi Maliseni .wabvala kabudura woyera.
Uyu ndi Maliseni. Ali kupephelera cakudya.
Uyu ndi Maliseni .Ali kupita ku chalichi.
Uyu ndi Maliseni .Ali kusuka mkamwa ndi mswaci.
Uyu ndi Maliseni .Ali ndi mlongo wace.
Uyu ndi Maliseni. Ali kupita kumsika kukagula ndiwo.
Uyu ndi Maliseni .Ali kuumba mbiya.
Uyu ndi Maliseni .Ali kupukuta ku maso.
Uyu ndi Maliseni .Ali kuthamanga.
Uyu ndi Maliseni .Ali kupukuta pa bolodi.