Ndikonda kujupha.
Ndikonda kuyenda mumvula.
Ndikonda kuyenda ndi ndodo.
Ndikonda kuuluka muphepo.
Ndikonda kuliza banjo.
Ndikonda kuthawa njoka.
Ndikonda kukwela bwato.
Ndikonda kukhala kujoko.
Ndikonda kuuluka mumlengalenga.
Ndikonda ugudubuka ngati nda thamanga kwambiri.
Ndikonda kupemphera.
Ndikonda kuwerenga.
Ndikonda kusambira.
Ndikonda kugwira nyama.
Ndikonda kuikira madzira.
Ndikonda kukumba mbewa.
Ndikonda kuweta tsitsi.