Onani amalume ali gone pa kama.
Onani mnyamata mubokosi ya milandu.
Onani mnyamata wanyamila pulanga yo khubvulira.
Onani nkhuku yagwira mbewa ndi mlomo wace.
Onani buluzi akuyenda m'madzi.
Onani mnyamata akulankhula pa lamya ndi kulemba.
Onani mbalame ikumwa madzi pa cikaye.
Onani poto uli pa moto.
Onani mnyamata akuthamanga kwambiri.
Onani fulu akudya udzu.
Onani njoka yalavula mata.
Onani atate anyamula futi.