Kodi ndine ndani? Ndine njoka.
Kodi ndine ndani? Ndine apo.
Kodi ndine ndani? Ndine mwezi.
Kodi ndine ndani? Ndine khasu.
Kodi ndine ndani? Ndine mtengo.
Kodi ndine ndani? Ndine thebulo.
Kodi ndine ndani? Ndine poto.
Kodi ndine ndani? Ndine nsomba.
Kodi ndine ndani? Ndine cimate.
Kodi ndine ndani? Ndine nthoci.
Kodi ndine ndani? Ndine mabuku.
Kodi ndine ndani? Ndine papaya.
Kodi ndine ndani? Ndine hala.
Kodi ndine ndani? Ndine Nkhwangwa.
Kodi ndine ndani? Ndine tiyi.
Kodi ndine ndani? Ndine nyumba ya udzu.