Kodi Tambala Alikucita Ciani?
IMPACT NETWORK and JOSEPH PHIRI

Tambala alikumwa madzi.

1

Tambala ali kumenya Mpira.

2

Tambala alikumanga ng'ombe.

3

Tambala alikuwedza nsomba.

4

Tambala alikuphika nsima.

5

Tambala alikutuma uthenga pa lampya.

6

Tambala alikusesa pabwalo.

7

Tambala alikudula mitengo.

8

Tambala alikulemba manambala.

9

Tambala alikulima.

10
You are free to download, copy, translate or adapt this story and use the illustrations as long as you attribute in the following way:
Kodi Tambala Alikucita Ciani?
Author - IMPACT NETWORK and JOSEPH PHIRI
Illustration -
Language - CiNyanja
Level - First paragraphs