Tikonda kuphika.
Tikonda kupemphera.
Tikonda kukwera njinga.
Tikonda kutapa madzi pa boho.
Tikonda kusenga mkaka.
Tikonda masewera olumpha.
Tikonda kusamba m'manja.
Tikonda kusema mithiko ndi mitondo.
Tikonda kujambula.
Tikonda kupanga zinthu monga: zisote, mphasa ndi malamba.
Tikonda kuphunzira.
Tikonda kuwerenga.
Tikonda kutunga madzi my m'tsinje.
Tikonda kumvetsera ku wailesi.
Tikonda kulima.
Tikonda kupenyelera wailesi wakanema.