Zinthu Zomwe Tikonda
IMPACT NETWORK and DAILESS ZULU

Tikonda kunyaya.

1

Tikonda kusewera masewera a mpira.

2

Tikonda kukhwapa maudzu.

3

Tikonda kuumba zinthu.

4

Tikonda kuyenda.

5

Tikonda ana.

6

Tikonda kulima.

7

Tikonda kunyololoka.

8

Tikonda kuphika.

9

Tikonda wailesi yakanema.

10

Tikonda kuwala kwa dzuwa.

11

Tikonda kuthamanga.

12

Tikonda kumanaga mabuluku ndi lamba wa cikasu.

13

Tikonda zomera.

14

Tikonda nyama zakuchire.

15

Tikonda dzanja lathu.

16

Tikonda kabudula wa msipu.

17

Tikonda ndembela ya dziko lathu LA Zambian.

18
You are free to download, copy, translate or adapt this story and use the illustrations as long as you attribute in the following way:
Zinthu Zomwe Tikonda
Author - IMPACT NETWORK and DAILESS ZULU
Illustration -
Language - CiNyanja
Level - First words