Ine ndine mkango. Ndimakhala kuthengo.
Ine ndine cule. Ndimakhala m'madzi.
Ine ndine kalulu. Ndimakhala kuthengo.
Ine ndine njoka. Ndimakhala kuthengo.
Ine ndine mbidzi. Ndimakhala kuthengo.
Ine ndine njati. Ndimakhala kuthengo.
Ine ndine nkhwazi. Ndimakhala kuthengo.
Ine ndine ng'ombe. Ndimakhala m'mudzi.
Ine ndine nkhosa. Ndimakhala m'mudzi.
Ine ndine galu. Ndimakhala m'mudzi.
Ine ndine mbewa. Ndimakhala kuthengo.
Ine ndine nyamalikiti. Ndimakhala kuthengo.
Ine ndine ng'ona. Ndimakhala m'madzi.
Ine ndine nkhunda. Ndimakhola m'mudzi.
Ine ndine nsomba. Ndimakhala m'madzi.
Ine ndine tambala. Ndimakhala m'mudzi.
Ine ndine nkhumba. Ndimakhala m'mudzi.
Ine ndine buluzi. Ndimakhala kuthengo.